Salimo 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithu, masiku onse a moyo wanga ndidzasangalala ndi ubwino wanu komanso chikondi chanu chokhulupirika,+Ndipo ndidzakhala mʼnyumba ya Yehova kwa moyo wanga wonse.+
6 Ndithu, masiku onse a moyo wanga ndidzasangalala ndi ubwino wanu komanso chikondi chanu chokhulupirika,+Ndipo ndidzakhala mʼnyumba ya Yehova kwa moyo wanga wonse.+