Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 17:45, 46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Davide anayankha Mfilisitiyo kuti: “Iwe ukubwera kudzamenyana ndi ine ndi lupanga, mkondo ndi nthungo,+ koma ine ndikubwera kudzamenyana nawe mʼdzina la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,+ Mulungu wa asilikali a Isiraeli, amene iweyo wamunyoza.+ 46 Lero Yehova akupereka mʼmanja mwanga,+ ndipo ndikupha nʼkukudula mutu. Lero ndipereka mitembo ya asilikali amʼmisasa ya Afilisiti kwa mbalame zamumlengalenga ndi kwa zilombo zakutchire. Anthu onse apadziko lapansi adzadziwa kuti Aisiraeli ali ndi Mulungu.+

  • 2 Samueli 21:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno panayambikanso nkhondo pakati pa Afilisiti ndi Aisiraeli.+ Choncho Davide ndi atumiki ake anapita kukamenyana ndi Afilisiti, koma Davide anatopa kwambiri.

  • 2 Samueli 21:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Nthawi yomweyo Abisai+ mwana wa Zeruya anathandiza+ Davide ndipo anapha Mfilisitiyo. Zitatero asilikali a Davide anamulumbirira kuti: “Musamapitenso ndi ife kunkhondo.+ Musazimitse nyale ya Isiraeli.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena