Salimo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,Mwachititsa kuti ulemerero wanu ukhale pamwamba kuposa kumwamba!+ Yesaya 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa tsiku limenelo mudzanena kuti: “Yamikani Yehova, itanani pa dzina lake,Dziwitsani mitundu ya anthu ntchito zake.+ Lengezani kuti dzina lake ndi lokwezeka.+
8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,Mwachititsa kuti ulemerero wanu ukhale pamwamba kuposa kumwamba!+
4 Pa tsiku limenelo mudzanena kuti: “Yamikani Yehova, itanani pa dzina lake,Dziwitsani mitundu ya anthu ntchito zake.+ Lengezani kuti dzina lake ndi lokwezeka.+