-
Salimo 92:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
92 Ndi bwino kuyamika inu Yehova,+
Ndiponso kuimba nyimbo zotamanda dzina lanu, inu Wamʼmwambamwamba.
-
92 Ndi bwino kuyamika inu Yehova,+
Ndiponso kuimba nyimbo zotamanda dzina lanu, inu Wamʼmwambamwamba.