Salimo 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu odziwa dzina lanu adzakukhulupirirani.+Simudzasiya anthu amene amakufunafunani, inu Yehova.+ Miyambo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzina la Yehova ndi nsanja yolimba.+ Wolungama amathawira mmenemo ndipo amatetezedwa.*+
10 Anthu odziwa dzina lanu adzakukhulupirirani.+Simudzasiya anthu amene amakufunafunani, inu Yehova.+