-
2 Mbiri 20:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Iwo anayamba kukhala mʼdzikolo ndipo anakumangirani malo opatulika a dzina lanu+ nʼkunena kuti, 9 ‘Tsoka likatigwera, kaya lupanga, chiweruzo chowawa, mliri kapena njala, tiziima patsogolo pa nyumbayi ndi pamaso panu (popeza dzina lanu lili mʼnyumbayi)+ nʼkufuulira inu kuti mutithandize pa mavuto athu, ndipo inu muzitimva nʼkutipulumutsa.’+
-