Salimo 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sonyezani modabwitsa chikondi chanu chokhulupirika,+Inu Mpulumutsi wa anthu amene amathawira kudzanja lanu lamanjaKuthawa anthu amene akupandukirani.
7 Sonyezani modabwitsa chikondi chanu chokhulupirika,+Inu Mpulumutsi wa anthu amene amathawira kudzanja lanu lamanjaKuthawa anthu amene akupandukirani.