Salimo 18:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Iye amachita zazikulu kuti apulumutse mfumu yake,+Amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa wodzozedwa wake,+Kwa Davide ndi mbadwa* zake mpaka kalekale.+
50 Iye amachita zazikulu kuti apulumutse mfumu yake,+Amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa wodzozedwa wake,+Kwa Davide ndi mbadwa* zake mpaka kalekale.+