Salimo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nʼchifukwa chiyani anthu a mitundu ina akuchita zipolowe,Ndiponso nʼchifukwa chiyani mitundu ya anthu ikungʼungʼudza za chinthu chopanda pake?*+
2 Nʼchifukwa chiyani anthu a mitundu ina akuchita zipolowe,Ndiponso nʼchifukwa chiyani mitundu ya anthu ikungʼungʼudza za chinthu chopanda pake?*+