Luka 23:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Kenako Yesu anafuula mokweza mawu kuti: “Atate, ndikupereka mzimu wanga mʼmanja mwanu!”+ Atanena zimenezi anatsirizika.+ Aheberi 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene Khristu anali padzikoli,* anapereka mapemphero ochonderera ndiponso opempha, kwa amene akanatha kumupulumutsa ku imfa. Anapereka mapempherowa mofuula komanso akugwetsa misozi,+ ndipo anamumvera chifukwa ankaopa Mulungu.
46 Kenako Yesu anafuula mokweza mawu kuti: “Atate, ndikupereka mzimu wanga mʼmanja mwanu!”+ Atanena zimenezi anatsirizika.+
7 Pamene Khristu anali padzikoli,* anapereka mapemphero ochonderera ndiponso opempha, kwa amene akanatha kumupulumutsa ku imfa. Anapereka mapempherowa mofuula komanso akugwetsa misozi,+ ndipo anamumvera chifukwa ankaopa Mulungu.