Salimo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthu wonyozekayu anaitana ndipo Yehova anamva. Anamupulumutsa ku mavuto ake onse.+ Salimo 69:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Chifukwa Yehova akumvetsera osauka,+Ndipo sadzanyoza anthu ake amene agwidwa ukapolo.+