Salimo 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chilamulo cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa mphamvu.*+ Zikumbutso za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+ Salimo 51:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Bwezeretsani mwa ine chisangalalo chimene chimabwera chifukwa cha chipulumutso chanu.+Ndipatseni mtima wofunitsitsa kukumverani.*
7 Chilamulo cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa mphamvu.*+ Zikumbutso za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+
12 Bwezeretsani mwa ine chisangalalo chimene chimabwera chifukwa cha chipulumutso chanu.+Ndipatseni mtima wofunitsitsa kukumverani.*