Salimo 63:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+ Ine ndikulakalaka inu.*+ Ndalefuka* chifukwa cholakalaka inuMʼdziko louma komanso lopanda madzi, kumene sikumera chilichonse.+ Salimo 105:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Funafunani Yehova+ ndipo muzidalira mphamvu zake. Nthawi zonse muzimupempha kuti akuthandizeni.* Zefaniya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Funafunani Yehova,+ inu nonse ofatsa* apadziko lapansi,Amene mumatsatira malamulo ake olungama.* Yesetsani kukhala olungama, yesetsani kukhala ofatsa.* Mwina mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+
63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+ Ine ndikulakalaka inu.*+ Ndalefuka* chifukwa cholakalaka inuMʼdziko louma komanso lopanda madzi, kumene sikumera chilichonse.+
3 Funafunani Yehova,+ inu nonse ofatsa* apadziko lapansi,Amene mumatsatira malamulo ake olungama.* Yesetsani kukhala olungama, yesetsani kukhala ofatsa.* Mwina mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+