Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 31:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Simunandipereke mʼmanja mwa adani,

      Koma mwachititsa kuti ndiime pamalo otetezeka.*

  • Salimo 41:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Yehova adzamuteteza nʼkusunga moyo wake.

      Anthu ena adzaona kuti akusangalala,+

      Ndipo Mulungu sadzamupereka kwa adani ake.*+

  • Salimo 41:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mdani wanga akapanda kundigonjetsa nʼkufuula mosangalala,

      Ndidzadziwa kuti mukusangalala nane.+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena