2 Samueli 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu wanga ndi thanthwe langa,+ ine ndimathawira kwa iye,Iye ndi chishango changa,+ nyanga* yanga ya chipulumutso* ndi malo anga achitetezo.*+Komanso ndi malo anga othawirako,+ mpulumutsi wanga+ amene amandipulumutsa kwa anthu achiwawa. Salimo 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso amene amandipulumutsa.+ Mulungu wanga ndi thanthwe langa+ limene ndimathawirako,Iye ndi chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso* komanso malo anga othawirako otetezeka.*+
3 Mulungu wanga ndi thanthwe langa,+ ine ndimathawira kwa iye,Iye ndi chishango changa,+ nyanga* yanga ya chipulumutso* ndi malo anga achitetezo.*+Komanso ndi malo anga othawirako,+ mpulumutsi wanga+ amene amandipulumutsa kwa anthu achiwawa.
2 Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso amene amandipulumutsa.+ Mulungu wanga ndi thanthwe langa+ limene ndimathawirako,Iye ndi chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso* komanso malo anga othawirako otetezeka.*+