Ekisodo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa nthawiyo Mose ndi Aisiraeli anaimbira Yehova nyimbo iyi:+ “Ndiimbira Yehova, chifukwa walemekezeka kwambiri.+ Mahatchi ndi okwera pamahatchiwo wawaponyera mʼnyanja.+ 2 Samueli 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Davide analankhula ndi Yehova mawu a nyimbo iyi,+ pa tsiku limene Yehova anamupulumutsa kwa adani ake onse+ ndiponso mʼmanja mwa Sauli.+
15 Pa nthawiyo Mose ndi Aisiraeli anaimbira Yehova nyimbo iyi:+ “Ndiimbira Yehova, chifukwa walemekezeka kwambiri.+ Mahatchi ndi okwera pamahatchiwo wawaponyera mʼnyanja.+
22 Davide analankhula ndi Yehova mawu a nyimbo iyi,+ pa tsiku limene Yehova anamupulumutsa kwa adani ake onse+ ndiponso mʼmanja mwa Sauli.+