Salimo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nʼchifukwa chake oipa sadzalephera kulangidwa,+Ndipo ochimwa sadzapezekanso pamene pali olungama.+