2 Samueli 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Munthu wokhulupirika, mumamuchitira mokhulupirika.+Munthu wamphamvu komanso wosalakwa, mumamuchitira mwachilungamo.+
26 Munthu wokhulupirika, mumamuchitira mokhulupirika.+Munthu wamphamvu komanso wosalakwa, mumamuchitira mwachilungamo.+