Salimo 37:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu amene Mulungu wawadalitsa adzalandira dziko lapansi,Koma amene wawatemberera adzaphedwa.+