Esitere 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Hamani anayamba kudzitama kuti ali ndi chuma chambiri, ana aamuna ambiri+ ndiponso kuti mfumu inamukweza pa udindo kuposa akalonga ndi atumiki ena onse a mfumuyo.+ Yobu 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nʼchifukwa chiyani oipa amakhalabe ndi moyo,+Amakalamba komanso amalemera* kwambiri?+
11 Ndiyeno Hamani anayamba kudzitama kuti ali ndi chuma chambiri, ana aamuna ambiri+ ndiponso kuti mfumu inamukweza pa udindo kuposa akalonga ndi atumiki ena onse a mfumuyo.+