Ekisodo 15:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mdaniyo anati: ‘Ndiwathamangira nʼkuwapeza! Ndigawa chuma chawo mpaka nditakhutira! Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+ 10 Mwapemerera mpweya wanu, ndipo nyanja yawamiza.+Amira mʼmadzi akuya ngati chitsulo cholemera.
9 Mdaniyo anati: ‘Ndiwathamangira nʼkuwapeza! Ndigawa chuma chawo mpaka nditakhutira! Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+ 10 Mwapemerera mpweya wanu, ndipo nyanja yawamiza.+Amira mʼmadzi akuya ngati chitsulo cholemera.