Salimo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma si mmene oipa alili.Iwo ali ngati mankhusu* amene amauluzika ndi mphepo. Miyambo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zabwino zimene munthu wolungama ankachita zikakumbukiridwa* amadalitsidwa,+Koma dzina la anthu oipa lidzawola.+ 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zimenezi zikusonyeza kuti Yehova* amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasunga kuti adzawawononge pa tsiku lopereka chiweruzo,+
7 Zabwino zimene munthu wolungama ankachita zikakumbukiridwa* amadalitsidwa,+Koma dzina la anthu oipa lidzawola.+
9 Zimenezi zikusonyeza kuti Yehova* amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasunga kuti adzawawononge pa tsiku lopereka chiweruzo,+