Yesaya 46:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale mudzakalambe, ine ndidzakhala chimodzimodzi.+Ngakhale tsitsi lanu lidzachite imvi, ine ndidzapitiriza kukunyamulani. Ndidzakunyamulani, kukuthandizani komanso kukupulumutsani ngati mmene ndakhala ndikuchitira.+ 1 Akorinto 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe mayesero amene mwakumana nawo osiyana ndi amene anthu ena amakumana nawo.+ Koma Mulungu ndi wokhulupirika ndipo sadzalola kuti muyesedwe kufika pamene simungapirire,+ koma pamene mukukumana ndi mayeserowo iye adzapereka njira yopulumukira kuti muthe kuwapirira.+
4 Ngakhale mudzakalambe, ine ndidzakhala chimodzimodzi.+Ngakhale tsitsi lanu lidzachite imvi, ine ndidzapitiriza kukunyamulani. Ndidzakunyamulani, kukuthandizani komanso kukupulumutsani ngati mmene ndakhala ndikuchitira.+
13 Palibe mayesero amene mwakumana nawo osiyana ndi amene anthu ena amakumana nawo.+ Koma Mulungu ndi wokhulupirika ndipo sadzalola kuti muyesedwe kufika pamene simungapirire,+ koma pamene mukukumana ndi mayeserowo iye adzapereka njira yopulumukira kuti muthe kuwapirira.+