Salimo 38:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ine ndakhala ngati munthu wogontha ndipo sindikumvetsera,+Ndakhala ngati munthu wosalankhula ndipo sindikutsegula pakamwa.+ Mateyu 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma pamene ansembe aakulu komanso akulu ankamuneneza, iye sanayankhe chilichonse.+ 1 Petulo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene anthu ankamunenera zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene ankazunzidwa,+ sanaopseze anthu amene ankamuzunzawo. Koma anasiya zonse mʼmanja mwa Woweruza amene amaweruza+ mwachilungamo.
13 Koma ine ndakhala ngati munthu wogontha ndipo sindikumvetsera,+Ndakhala ngati munthu wosalankhula ndipo sindikutsegula pakamwa.+
23 Pamene anthu ankamunenera zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene ankazunzidwa,+ sanaopseze anthu amene ankamuzunzawo. Koma anasiya zonse mʼmanja mwa Woweruza amene amaweruza+ mwachilungamo.