Salimo 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha dzina lanu, inu Yehova,+Mundikhululukire tchimo langa, ngakhale kuti ndi lalikulu. Mika 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzagonjetsa* zolakwa zathu. Machimo athu onse mudzawaponya mʼnyanja pamalo ozama.+
19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzagonjetsa* zolakwa zathu. Machimo athu onse mudzawaponya mʼnyanja pamalo ozama.+