Luka 24:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ndiyeno anawauza kuti: “Pamene ndinali nanu limodzi ndinakuuzani mawu akuti,+ zonse zokhudza ine zimene zinalembedwa mʼChilamulo cha Mose, zimene aneneri analemba komanso zimene zinalembedwa mʼMasalimo ziyenera kukwaniritsidwa.”+
44 Ndiyeno anawauza kuti: “Pamene ndinali nanu limodzi ndinakuuzani mawu akuti,+ zonse zokhudza ine zimene zinalembedwa mʼChilamulo cha Mose, zimene aneneri analemba komanso zimene zinalembedwa mʼMasalimo ziyenera kukwaniritsidwa.”+