Salimo 35:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma amene amakonda chilungamo changa afuule mosangalala.Nthawi zonse azinena kuti: “Alemekezeke Yehova, amene amasangalala mtumiki wake akakhala pamtendere.”+
27 Koma amene amakonda chilungamo changa afuule mosangalala.Nthawi zonse azinena kuti: “Alemekezeke Yehova, amene amasangalala mtumiki wake akakhala pamtendere.”+