Salimo 143:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyankheni mofulumira, inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.*+ Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+
7 Ndiyankheni mofulumira, inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.*+ Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+