Salimo 72:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale,+Ndipo lipitirize kutchuka kwa nthawi zonse pamene dzuwa lidzakhalepo. Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.+Mitundu yonse ya anthu imutchule kuti ndi wosangalala.
17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale,+Ndipo lipitirize kutchuka kwa nthawi zonse pamene dzuwa lidzakhalepo. Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.+Mitundu yonse ya anthu imutchule kuti ndi wosangalala.