Deuteronomo 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyendayenda mumsasa wanu+ kuti akupulumutseni ndi kupereka adani anu mʼmanja mwanu. Choncho msasa wanu uzikhala woyera,+ kuti asaone choipa chilichonse pakati panu nʼkusiya kuyenda nanu limodzi. Salimo 132:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa Yehova wasankha Ziyoni.+Akufunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye akuti:+ Yesaya 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Fuulani mwachisangalalo inu okhala mu Ziyoni,*Chifukwa Woyera wa Isiraeli amene ali pakati panu ndi wamkulu.”
14 Chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyendayenda mumsasa wanu+ kuti akupulumutseni ndi kupereka adani anu mʼmanja mwanu. Choncho msasa wanu uzikhala woyera,+ kuti asaone choipa chilichonse pakati panu nʼkusiya kuyenda nanu limodzi.
6 Fuulani mwachisangalalo inu okhala mu Ziyoni,*Chifukwa Woyera wa Isiraeli amene ali pakati panu ndi wamkulu.”