Deuteronomo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu. Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, pa anthu onse okhala padziko lapansi.+ Malaki 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wanena kuti: “Ine ndimakukondani anthu inu.”+ Koma inu mwanena kuti: “Mwasonyeza bwanji kuti mumatikonda?” “Kodi Esau sanali mchimwene wake wa Yakobo?+ Koma ine ndinakonda Yakobo,” watero Yehova.
6 Chifukwa ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu. Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, pa anthu onse okhala padziko lapansi.+
2 Yehova wanena kuti: “Ine ndimakukondani anthu inu.”+ Koma inu mwanena kuti: “Mwasonyeza bwanji kuti mumatikonda?” “Kodi Esau sanali mchimwene wake wa Yakobo?+ Koma ine ndinakonda Yakobo,” watero Yehova.