Miyambo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chuma chidzakhala chopanda* phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+Koma chilungamo nʼchimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+ Mateyu 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kodi munthu angapindule chiyani ngati atapeza zinthu zonse zamʼdzikoli koma nʼkutaya moyo wake?+ Kapena kodi munthu angapereke chiyani choti asinthanitse ndi moyo wake?+
4 Chuma chidzakhala chopanda* phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+Koma chilungamo nʼchimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+
26 Kodi munthu angapindule chiyani ngati atapeza zinthu zonse zamʼdzikoli koma nʼkutaya moyo wake?+ Kapena kodi munthu angapereke chiyani choti asinthanitse ndi moyo wake?+