Salimo 49:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu amene sazindikira zimenezi, ngakhale atakhala wolemekezeka,+ Amangofanana ndi nyama zimene zimafa.
20 Munthu amene sazindikira zimenezi, ngakhale atakhala wolemekezeka,+ Amangofanana ndi nyama zimene zimafa.