Yesaya 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi mudzatani pa tsiku lachiweruzo,*+Anthu okuwonongani akadzabwera kuchokera kutali?+ Kodi mudzathawira kwa ndani kuti akuthandizeni+Nanga chuma* chanu mudzachisiya kuti?
3 Kodi mudzatani pa tsiku lachiweruzo,*+Anthu okuwonongani akadzabwera kuchokera kutali?+ Kodi mudzathawira kwa ndani kuti akuthandizeni+Nanga chuma* chanu mudzachisiya kuti?