-
Rute 3:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Atatero, Boazi anati: “Yehova akudalitse mwana wanga. Chikondi chokhulupirika chimene wasonyeza panopa chikuposa choyamba chija,+ chifukwa sunafune anyamata, kaya osauka kapena olemera. 11 Ndiye tamvera mwana wanga, usachite mantha. Ndikuchitira zonse zimene wanena,+ chifukwa aliyense mumzindawu akudziwa kuti ndiwe mkazi wabwino kwambiri.
-