Miyambo 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakamwa pa akazi amakhalidwe oipa* pali ngati dzenje lakuya.+ Amene waputa mkwiyo wa Yehova adzagweramo.
14 Pakamwa pa akazi amakhalidwe oipa* pali ngati dzenje lakuya.+ Amene waputa mkwiyo wa Yehova adzagweramo.