Miyambo 6:12, 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu wopanda pake komanso woipa, amangoyendayenda nʼkumalankhula mabodza.+13 Amatsinzinira ena diso lake,+ amachita zizindikiro ndi phazi lake ndiponso amachita zizindikiro ndi zala zake.
12 Munthu wopanda pake komanso woipa, amangoyendayenda nʼkumalankhula mabodza.+13 Amatsinzinira ena diso lake,+ amachita zizindikiro ndi phazi lake ndiponso amachita zizindikiro ndi zala zake.