Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 18:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako Sauli anauza Davide kuti: “Paja ndili ndi mwana wamkazi wamkulu, Merabu,+ ndipo ndidzakupatsa kuti akhale mkazi wako.+ Koma iweyo upitirize kumenya nkhondo za Yehova+ ndiponso kundisonyeza kuti ndiwe wolimba mtima.” Mumtima mwake ankati: ‘Ndisamuphe ndine koma amuphe ndi Afilisiti.’+

  • 1 Samueli 18:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Choncho Sauli anati: “Ndimʼpatsa Mikala kuti akhale msampha kwa iye, kuti Afilisiti amuphe.”+ Zitatero Sauli anauzanso Davide kachiwiri kuti: “Lero uchita nane mgwirizano wa ukwati.”*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena