Yeremiya 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzakupatsani abusa amene amachita zinthu zogwirizana ndi zofuna zanga+ ndipo adzakuthandizani kuti mudziwe zinthu zambiri ndiponso kuti mukhale omvetsa zinthu.
15 Ndidzakupatsani abusa amene amachita zinthu zogwirizana ndi zofuna zanga+ ndipo adzakuthandizani kuti mudziwe zinthu zambiri ndiponso kuti mukhale omvetsa zinthu.