Miyambo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzina la Yehova ndi nsanja yolimba.+ Wolungama amathawira mmenemo ndipo amatetezedwa.*+ Yesaya 40:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma anthu amene amayembekezera Yehova adzapezanso mphamvu. Iwo adzaulukira mʼmwamba ngati kuti ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka.Adzayenda koma osatopa.”+
31 Koma anthu amene amayembekezera Yehova adzapezanso mphamvu. Iwo adzaulukira mʼmwamba ngati kuti ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka.Adzayenda koma osatopa.”+