-
Miyambo 6:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Mwana wanga, ngati walonjeza kuti udzapereka ngongole ya mnzako iye akadzalephera kubweza,+
Ngati wagwirana dzanja ndi mlendo pochita mgwirizano,+
-
Miyambo 6:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Dzipulumutse ngati insa mʼmanja mwa wosaka,
Ndiponso ngati mbalame mʼmanja mwa wosaka mbalame.
-
-
-