Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 25:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Davide atamva kuti Nabala wamwalira ananena kuti: “Adalitsike Yehova amene wandiweruzira mlandu+ wa mawu onyoza a Nabala,+ komanso wandiletsa ine mtumiki wake kuti ndisachite choipa chilichonse.+ Yehova wabwezera zoipa za Nabala pamutu pake!” Kenako Davide anatuma anthu kuti akamufunsirire Abigayeli kuti akhale mkazi wake.

  • 1 Petulo 3:3, 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kudzikongoletsa kwanu kusakhale kwa kunja kokha monga kumanga tsitsi, kuvala zodzikongoletsera zagolide+ kapena zovala zapamwamba. 4 Koma kukhalenso kwa munthu wobisika mumtima, atavala zovala zosawonongeka, zomwe ndi mtima wodekha komanso wofatsa+ umene ndi wamtengo wapatali pamaso pa Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena