-
Yakobo 5:3, 4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Golide ndi siliva wanu wawonongeka ndi dzimbiri. Dzimbiri limenelo lidzakhala umboni wokutsutsani ndipo lidzadya mnofu wanu. Zimene mwasunga zidzakhala ngati moto mʼmasiku otsiriza.+ 4 Tamverani! Malipiro amene simunapereke kwa anthu amene anagwira ntchito yokolola mʼminda yanu akufuula ndipo Yehova* wa magulu ankhondo akumwamba wamva kufuula kopempha thandizo kwa anthu okololawo.+
-