Yobu 27:13, 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ili ndi gawo la munthu woipa lochokera kwa Mulungu,+Cholowa chimene anthu ozunza anzawo amalandira kuchokera kwa Wamphamvuyonse. 14 Ana ake akachuluka, adzaphedwa ndi lupanga,+Ndipo mbadwa zake sizidzakhala ndi chakudya chokwanira.
13 Ili ndi gawo la munthu woipa lochokera kwa Mulungu,+Cholowa chimene anthu ozunza anzawo amalandira kuchokera kwa Wamphamvuyonse. 14 Ana ake akachuluka, adzaphedwa ndi lupanga,+Ndipo mbadwa zake sizidzakhala ndi chakudya chokwanira.