Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 31:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ngati ndikudalira golide,

      Kapena kuuza golide woyenga bwino kuti, ‘Ndimadalira iwe.’+

  • Yobu 31:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Chimenecho chikanakhala cholakwa chimene oweruza akuyenera kundipatsira chilango,

      Chifukwa ndikanakhala nditakana Mulungu woona wakumwamba.

  • Salimo 52:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Nʼchifukwa chake Mulungu adzakugwetsa ndipo sudzakhalakonso.+

      Adzakugwira nʼkukukokera kutali ndi tenti yako,+

      Ndipo adzakuzula nʼkukuchotsa mʼdziko la anthu amoyo.+ (Selah)

  • Salimo 52:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 “Taonani, munthu uyu sanadalire Mulungu monga malo ake othawirako,*+

      Koma ankadalira chuma chake chochuluka,+

      Komanso ziwembu zimene ankapanga.”*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena