-
Genesis 41:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Kenako Farao anauza Yosefe kuti: “Popeza kuti Mulungu wakudziwitsa zonsezi, palibenso munthu wina wozindikira ndi wanzeru ngati iwe.
-