Miyambo 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pali munthu amene amadzionetsa ngati wolemera koma chonsecho alibe chilichonse.+Pali munthu winanso amene amadzionetsa ngati wosauka koma ali ndi chuma chambiri.
7 Pali munthu amene amadzionetsa ngati wolemera koma chonsecho alibe chilichonse.+Pali munthu winanso amene amadzionetsa ngati wosauka koma ali ndi chuma chambiri.