Salimo 37:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pewani kuchita zoipa ndipo muzichita zabwino,+Mukatero mudzakhala padziko lapansi mpaka kalekale. Miyambo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zabwino zimene munthu wolungama ankachita zikakumbukiridwa* amadalitsidwa,+Koma dzina la anthu oipa lidzawola.+ Habakuku 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Taona munthu wodzikuza,Mtima wake si wowongoka. Koma wolungama adzakhala ndi moyo chifukwa cha kukhulupirika kwake.*+
7 Zabwino zimene munthu wolungama ankachita zikakumbukiridwa* amadalitsidwa,+Koma dzina la anthu oipa lidzawola.+
4 Taona munthu wodzikuza,Mtima wake si wowongoka. Koma wolungama adzakhala ndi moyo chifukwa cha kukhulupirika kwake.*+