Miyambo 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Munthu waulesi adzakhala wosauka,+Koma wogwira ntchito mwakhama adzalemera.+ Miyambo 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dzanja la anthu akhama lidzalamulira anthu,+Koma manja aulesi adzagwira ntchito yokakamiza.+