Oweruza 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako amuna a ku Efuraimu anamʼfunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani watichitira zimenezi? Bwanji sunatiitane pokamenyana ndi Amidiyani?”+ Ndipo iwo anakangana naye kwambiri.+
8 Kenako amuna a ku Efuraimu anamʼfunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani watichitira zimenezi? Bwanji sunatiitane pokamenyana ndi Amidiyani?”+ Ndipo iwo anakangana naye kwambiri.+